Zowonera

Mneneri Wa Mu Zaka Zana Za Makumi Awiri, imene inajambulidwa mu kala, ikukubweretsani inu ku nyumba ya M’bale Branham pa zolankhulana zapadera mu 1953.

Msonkhano Wokopa anthu waku Chicago inajambulidwa mu Chicago, Illinois mu Ogasiti, 1953.

Kuya Kuyitanira Ku Kuya inajambulidwa mu Constitution Hall mu Washington, D.C, mu Juni wa 1954