Baibulo limanena kuti, “Kotero chikhulupiriro chimadza pakumva, ndipo pakumva Mawu a Mulungu.” (Aroma 10:17). Ukamamvetsera kwambiri ku Mawu, ndi pamene umakhala ndi chikhulupiriro chochuluka. Maulaliki otsatirawa ndi tizidutswa pang’ono ta mazana omwe ife tiri nawo.